Hot Current pa nkhani ya a Chakwera kupitilira kukhala mtsogoleri wa MCP – 26 October 2025

Posted on 10/27/2025
|

Brian Banda, Bayana Chunga ndi Wonder Msiska kukambirana za a Chakwera kuti apitilira kukhala mtsogoleri wa MCP, opikisana mu ofesi ya usipika adziwika tsopano, komanso a Mutharika akuti nduna zizipereka malipoti pa mwezi.