Hot Current pa nkhani ya chisankho chapa 16 September – 14 September 2025

Posted on 09/15/2025
|

Brian Banda, Cathy Maulidi ndi Wonder Msiska kukambirana za chisankho chomwe chili pa 16 September, mmene Amalawi akuyenera kuchitira.