Leah Malekano ndi Wonder Msiska kukambirana za lamulo 74 ndi 75 lomwe ladutsa ku nyumba yamalamulo lolora, anthu otumidwa ndi Mec kukavotera malo omwe akugwilira ntchito nthawi yachisankho
Kulinji pa lamulo la gawo 74 ndi 75 kunyumba yamalamulo – 6 August 2025
Posted on 08/06/2025