Kulinji pa nkhani ya kuyimanso kwa a Peter Mutharika – 18 June 2025

Posted on 06/18/2025
|

Fungai Mutsinze ndi Wonder Msiska kukambirana nkhani yokhudza kuyimanso kwa a Peter Mutharika pachisankho cha mtsogoleri wa dziko lino