Hot Current – 16 March 2025

Posted on 03/17/2025
|

Wonder Msiska, Bayana Chunga ndi Jonah Pankuku kukambirana za miyezi 6 yomwe yatsala kuti tiponye voti ndi maphunziro omwe Malawi angapeze pa mmene Donald Trump akuchitira zinthu.