Kulinji pa nkhani ya ziwonetsero – 2 July 2025

Posted on 07/02/2025
|

Leah Malekano ndi Wonder Msiska kukambirana nkhani yokhudza ziwonetsero zomwe akonza a Alfred Gangata, pofuna kuwonetsa kusakondwa pa momwe zinthu zikukhalira mdziko muno