Kulinji pa nkhani ya mtsutso wa atsogoleri azipani – 9 September 2025

Posted on 09/09/2025
|

Davie Gadama ndi Innocent Mphongolo kukambirana nkhani ya mtsutso wa atsogoleri azipani omwe wakonzedwa lero ku BICC, ndi chifukwa chani atsogoleri ena samapita