Kulinji pa nkhani ya thumba la Constituency Development Fund – 28 October 2025

Posted on 10/28/2025
|

Leah Malekano ndi Innocent Mphongolo kukambirana za tsogolo la thumba la Constituency Development Fund pamene nyumba ya malamulo iyambe zokambirana sabata ino