Kanema kuonetsa mmene zinaliri ku bwalo la Chief Resident Magistrate mu mzinda wa Lilongwe kumene bwaloli lidapereka chigamulo chake pa mlandu wokhudza mneneri Shepherd Bushiri ndi akazi awo a Mary Bushiri.
Shepherd Bushiri ku bwalo la Chief Resident Magistrate – 12 March 2025
Posted on 03/12/2025
|