Kulinji pa nkhani ya katangale Mmalawi – 2 September 2025

Posted on 09/02/2025
|

Leah Malekano ndi Innocent Mphongolo kukambirana nkhani ya katangale amene mtsogoleri wa Odya Zake Alibe Mulandu, Michael Usi, akunena kuti wachuluka mboma, pamene kwatsala masaba awiri kuti Amalawi asankhe atsogoleri atsopano