Sports Arena kuwunikira mpikisano wa FDH Bank – 17 October 2025

Posted on 10/18/2025
|

Williams Gondwa ndi Mike Ndala kukambirana za mpikisano wa FDH Bank Cup wa 2025, masewero a mpira wa atsikana wapakati pa Silver Strikers Ladies ndi FCB Nyasa Big Bullets, mwa zina