Williams Gondwa kukambirana ndi Mike Ndala za mwayi wa akatswiri a Flames, Yankho Singo amene akukasewera ku Golden Arrows ku South Africa ndi Chimwemwe Idana amene akukasewera ku Zanaco ku Zambia, mwa nkhani zina
Sports Arena pa mwayi wa akatswiri a Flames – 27 June 2025
Posted on 06/28/2025
|