Danga Langa pa nkhani ya mlatho wa Kabula – 14 May 2025

Posted on 05/15/2025
|

Mu Danga Langa lero, Isaac Salima kucheza ndi anthu okhala ku Mbayani mu mzinda wa Blantyre pamalo pomwe pakumangidwa mlatho wa Kabula, mmene kuonongeka kwa mlatho kwawakhudzira