Mtedza Mtedza kucheza ndi Moses Mkondowe – 6 August 2025

Posted on 08/07/2025
|

Peter Fote wa Mtedza Mtedza Sports kucheza ndi Moses MKondowe, mphunzitsi wa Tauka Athletics Club, pamalingaliro owumba othamanga omwe adzakwanitse kupita ku mpikisano wa Olympic mtsogolomu