Mtedza Mtedza Sports kucheza ndi Steve Liwewe Banda – 2 July 2025

Posted on 07/03/2025
|

Isaac Salima wa Mtedza Mtedza Sports kucheza ndi Steve Liwewe Banda, katswiri onenelera masewero a mpira, mmene anayambira ntchitoyi, ndi mmene ulendo wakhalira kufikila lero