Sports Arena kuwunikira mpikisano wa TNM Super League – 27 October 2025

Posted on 10/28/2025
|

Peter Fote, Francis Pata ndi Mike Ndala kukambirana za masewero a FCB Nyasa Big Bullets ndi Mighty Wanderers mu TNM Super League komanso masewero a Scorchers, mwa nkhani zina