Mtedza Mtedza kucheza ndi Francis Spata – 22 October 2025

Posted on 10/23/2025
|

Peter Fote wa Mtedza Mtedza Sports kucheza ndi Francis Spata, mtola nkhani wamasewero, kuwunikira kuti ndi ndani angatenge ukastwiri wa league ya TNM ya chaka chino