Kulinji pa nkhani ya ndalama yomwe Cosoma yalipira anthu aluso – 13 August 2025

Posted on 08/13/2025
|

Leah Malekano ndi Bayana Chunga kukambirana nkhani ya K1.5 billion yomwe Cosoma yalipira anthu aluso, pomwe ena alandira zochuluka, ena alandira zochepa