Kulinji pa nkhani ya zomwe anayankhula Peter Mutharika – 22 October 2025

Posted on 10/22/2025
|

Leah Malekano ndi Bayana Chunga kukambirana zomwe anayankhula Mtsogoleri wa dziko lino Peter Mutharika kumwambo olumbilitsa wachiwiri wina kwa mtsogoleri wa dziko lino a Enoch Chihana