Mtedza Mtedza kucheza ndi Christopher Gototo – 29 October 2025

Posted on 10/31/2025
|

Peter Fote wa Mtedza Mtedza kucheza ndi Christopher Gototo, wosewera mpira wamiyendo, kuwunikira ulendo wake wa mpira, kuwesera ma timu 6 muzaka zitatu, mwa nkhani zina