Hot Current pa nkhani ya atsogoleri atsopano adziko – 19 October 2025

Posted on 10/20/2025
|

Wonder Msiska ndi Bayana Chunga kukambirana za nduna zina ziwiri zomwe mtsogoleri wa dziko lino wasankha komanso kutsegulidwa kwa Nyumba ya Malamulo.