Kulinji pa nkhani ya migwirizano ya zipani – 12 August 2025

Posted on 08/12/2025
|

Leah Malekano ndi Innocent Mphongolo kukambirana nkhani ya migwirizano ya zipani za ndale pamene kwatsala masiku 35 kuti tsiku lachisankho lifike