Thyolo sings boma ndilomweri – 14 May 2025

Posted on 05/15/2025
|

Anthu a ku Thyolo anayimba nyimbo ya boma ndilomweri polandira wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi mmudzi wa Chilomo T/A Nanseta