Kulinji pa nkhani ya kuchotsedwa ntchito kwa ena mboma – 8 October 2025

Posted on 10/08/2025
|

Bayana Chunga ndi Wonder Msiska kukambirana ngati nkotheka kusintha mchitidwe wochotsa kapena kusintha ntchito kwa ena mwa ogwira ntchito mboma pamene ulamuliro wasintha