Kulinji pa nkhani ya bwana wamkulu wa MBC – 13 October 2025

Posted on 10/13/2025
|

Leah Malekano ndi Wanangwa Chafulumira kukambirana za zomwe zinachitika ku MBC pamene bwana wamkulu anachitiridwa za mtopola ndi anyamata a chipani