Kulinji pa nkhani ya zotsatira za chisankho – 8 September 2025

Posted on 09/08/2025
|

Leah Malekano ndi Wanangwa Chafulumira kukambirana ndi atsogoleri a MCP ndi DPP pa mmene akuwakonzekeletsera owatsatira awo kudzavomereza zotsatira za chisankho ngati adzapambane kapena kugonja