Kulinji pa nkhani ya aphungu atsopano – 21 October 2025

Posted on 10/21/2025
|

Leah Malekano ndi Innocent Mphongolo kukambirana za aphungu a nyumba ya malamulo atsopano amene ayamba zokonzekera kukumana kwawo