Kulinji pa nkhani ya ziwonetsero zotsutsana ndi mkulu wa Mec – 25 June 2025

Posted on 06/25/2025
|

Leah Malekano ndi Wonder Msiska kukambirana nkhani yokhudza anthu amene akufuna kupanga ziwonetsero pofuna kukakamiza mkulu wa Mec kutula pansi udindo wake